Maliko 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zitatero munthuyo ananyamuka ndipo nthawi yomweyo ananyamula machira akewo nʼkuyenda yekha pamaso pa anthu onse. Choncho onsewo anadabwa kwambiri ndipo anatamanda Mulungu kuti: “Zoterezi sitinazionepo.”+
12 Zitatero munthuyo ananyamuka ndipo nthawi yomweyo ananyamula machira akewo nʼkuyenda yekha pamaso pa anthu onse. Choncho onsewo anadabwa kwambiri ndipo anatamanda Mulungu kuti: “Zoterezi sitinazionepo.”+