Yohane 1:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 ndipo anapita naye kwa Yesu. Yesu atamuyangʼana anati: “Iwe ndiwe Simoni+ mwana wa Yohane, dzina lako likhala Kefa” (limene kumasulira kwake ndi “Petulo”).+ Machitidwe 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Sumiyoni+ wafotokoza bwino mmene Mulungu anacheukira anthu a mitundu ina kwa nthawi yoyamba, kuti pakati pawo atengepo anthu odziwika ndi dzina lake.+
42 ndipo anapita naye kwa Yesu. Yesu atamuyangʼana anati: “Iwe ndiwe Simoni+ mwana wa Yohane, dzina lako likhala Kefa” (limene kumasulira kwake ndi “Petulo”).+
14 Sumiyoni+ wafotokoza bwino mmene Mulungu anacheukira anthu a mitundu ina kwa nthawi yoyamba, kuti pakati pawo atengepo anthu odziwika ndi dzina lake.+