Mateyu 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Afarisi atamva zimenezi ananena kuti: “Ameneyutu sikuti amatulutsa ziwanda ndi mphamvu zake ayi koma ndi mphamvu za Belezebule,* wolamulira ziwanda.”+ Maliko 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komanso alembi amene anachokera ku Yerusalemu ankanena kuti: “Ali ndi Belezebule,* ndipo amatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya wolamulira ziwanda.”+ Luka 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ena mwa iwo ananena kuti: “Ameneyu amatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya Belezebule,* wolamulira ziwanda.”+ Yohane 8:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Ayudawo anamuyankha kuti: “Kodi tikunama tikamanena kuti, ‘Ndiwe Msamariya+ ndipo uli ndi chiwandaʼ?”+
24 Afarisi atamva zimenezi ananena kuti: “Ameneyutu sikuti amatulutsa ziwanda ndi mphamvu zake ayi koma ndi mphamvu za Belezebule,* wolamulira ziwanda.”+
22 Komanso alembi amene anachokera ku Yerusalemu ankanena kuti: “Ali ndi Belezebule,* ndipo amatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya wolamulira ziwanda.”+
15 Koma ena mwa iwo ananena kuti: “Ameneyu amatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya Belezebule,* wolamulira ziwanda.”+
48 Ayudawo anamuyankha kuti: “Kodi tikunama tikamanena kuti, ‘Ndiwe Msamariya+ ndipo uli ndi chiwandaʼ?”+