Luka 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Patatha masiku 8, nthawi yoti achite mdulidwe wa mwanayo itakwana,+ anamupatsa dzina lakuti Yesu. Limeneli ndi dzina limene mngelo uja anatchula Mariya asanakhale woyembekezera.+
21 Patatha masiku 8, nthawi yoti achite mdulidwe wa mwanayo itakwana,+ anamupatsa dzina lakuti Yesu. Limeneli ndi dzina limene mngelo uja anatchula Mariya asanakhale woyembekezera.+