Hoseya 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa ndimakondwera ndi chikondi chokhulupirika,* osati nsembe.Ndimakondweranso ndi kudziwa Mulungu, osati nsembe zopsereza zathunthu.+ Mika 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kodi nditenge chiyani popita kwa Yehova? Ndikagwade ndi chiyani kwa Mulungu wakumwamba? Kodi ndipite nditatenga nsembe zopsereza zathunthu?Ndiponso ana a ngʼombe achaka chimodzi?+ Mika 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye anakuuza munthu iwe zimene zili zabwino. Kodi Yehova akufuna kuti uzichita* chiyani? Iye akungofuna kuti uzichita chilungamo,*+ uziona kuti kukhulupirika nʼkofunika,*+Ndiponso uziyenda modzichepetsa+ ndi Mulungu wako.+ Mateyu 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho pitani mukaphunzire tanthauzo la mawu akuti: ‘Ndikufuna chifundo, osati nsembe.’+ Chifukwa ine sindinabwere kudzaitana anthu olungama, koma ochimwa.”
6 Chifukwa ndimakondwera ndi chikondi chokhulupirika,* osati nsembe.Ndimakondweranso ndi kudziwa Mulungu, osati nsembe zopsereza zathunthu.+
6 Kodi nditenge chiyani popita kwa Yehova? Ndikagwade ndi chiyani kwa Mulungu wakumwamba? Kodi ndipite nditatenga nsembe zopsereza zathunthu?Ndiponso ana a ngʼombe achaka chimodzi?+
8 Iye anakuuza munthu iwe zimene zili zabwino. Kodi Yehova akufuna kuti uzichita* chiyani? Iye akungofuna kuti uzichita chilungamo,*+ uziona kuti kukhulupirika nʼkofunika,*+Ndiponso uziyenda modzichepetsa+ ndi Mulungu wako.+
13 Choncho pitani mukaphunzire tanthauzo la mawu akuti: ‘Ndikufuna chifundo, osati nsembe.’+ Chifukwa ine sindinabwere kudzaitana anthu olungama, koma ochimwa.”