Mateyu 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Munthu aliyense akamva mawu a Ufumu koma osazindikira tanthauzo lake, woipayo+ amabwera nʼkuchotsa zimene zafesedwa mumtima wa munthuyo. Iyi ndi mbewu imene inafesedwa mʼmbali mwa msewu ija.+
19 Munthu aliyense akamva mawu a Ufumu koma osazindikira tanthauzo lake, woipayo+ amabwera nʼkuchotsa zimene zafesedwa mumtima wa munthuyo. Iyi ndi mbewu imene inafesedwa mʼmbali mwa msewu ija.+