Yohane 12:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Wachititsa khungu maso awo ndipo waumitsa mitima yawo, kuti asamaone ndi maso awowo, kuti mitima yawo isamvetse zinthu nʼkutembenuka kuti ine ndiwachiritse.”+ Aroma 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 ngati mmene Malemba amanenera kuti: “Mulungu wawapatsa mzimu wa tulo tofa nato,+ maso osaona ndi makutu osamva, mpaka lero.”+ 2 Akorinto 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo maganizo awo anachita khungu.+ Mpaka lero, nsaluyo imakhalabe yophimba pangano lakale likamawerengedwa,+ chifukwa imachotsedwa kudzera mwa Khristu basi.+
40 “Wachititsa khungu maso awo ndipo waumitsa mitima yawo, kuti asamaone ndi maso awowo, kuti mitima yawo isamvetse zinthu nʼkutembenuka kuti ine ndiwachiritse.”+
8 ngati mmene Malemba amanenera kuti: “Mulungu wawapatsa mzimu wa tulo tofa nato,+ maso osaona ndi makutu osamva, mpaka lero.”+
14 Ndipo maganizo awo anachita khungu.+ Mpaka lero, nsaluyo imakhalabe yophimba pangano lakale likamawerengedwa,+ chifukwa imachotsedwa kudzera mwa Khristu basi.+