Maliko 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Nthawi yomweyo anapita kwa mfumuyo mofulumira nʼkupempha kuti: “Ndikufuna mundipatse mutu wa Yohane Mʼbatizi mʼmbale pompano.”+
25 Nthawi yomweyo anapita kwa mfumuyo mofulumira nʼkupempha kuti: “Ndikufuna mundipatse mutu wa Yohane Mʼbatizi mʼmbale pompano.”+