Maliko 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atachoka kumeneko anapita mʼchigawo cha Turo ndi Sidoni.+ Kumeneko anakalowa mʼnyumba ina ndipo sanafune kuti aliyense adziwe kuti ali kumeneko. Koma anthu anadziwabe.
24 Atachoka kumeneko anapita mʼchigawo cha Turo ndi Sidoni.+ Kumeneko anakalowa mʼnyumba ina ndipo sanafune kuti aliyense adziwe kuti ali kumeneko. Koma anthu anadziwabe.