Yohane 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kunabwera munthu wina amene anatumidwa monga nthumwi ya Mulungu. Dzina lake anali Yohane.+