Mateyu 17:22, 23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Atasonkhana pamodzi ku Galileya, Yesu anawauza kuti: “Mwana wa munthu adzaperekedwa mʼmanja mwa anthu+ 23 ndipo adzamupha. Koma pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.”+ Atamva zimenezi iwo anamva chisoni kwambiri. Mateyu 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Muno mulibe chifukwa waukitsidwa mogwirizana ndi zimene ananena.+ Bwerani muone pamene anagona. Machitidwe 10:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ameneyu Mulungu anamuukitsa pa tsiku lachitatu+ nʼkulola kuti anthu amuone, 1 Akorinto 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiponso kuti anaikidwa mʼmanda,+ kenako anaukitsidwa+ pa tsiku lachitatu,+ mogwirizana ndi Malemba.+
22 Atasonkhana pamodzi ku Galileya, Yesu anawauza kuti: “Mwana wa munthu adzaperekedwa mʼmanja mwa anthu+ 23 ndipo adzamupha. Koma pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.”+ Atamva zimenezi iwo anamva chisoni kwambiri.
4 Ndiponso kuti anaikidwa mʼmanda,+ kenako anaukitsidwa+ pa tsiku lachitatu,+ mogwirizana ndi Malemba.+