Machitidwe 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anapha ndi lupanga+ Yakobo, mchimwene wake wa Yohane.+ Aroma 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho ngati tili ana, ndifenso olandira cholowa kuchokera kwa Mulungu. Koma ndifenso olandira cholowa+ anzake a Khristu, ngati tikuvutika naye limodzi+ kuti tikalandire naye ulemerero.+ 2 Akorinto 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chiyembekezo chathu pa inu sichikugwedezeka, chifukwa tikudziwa kuti popeza mukukumana ndi mavuto ofanana ndi amene ifeyo tikukumana nawo, nanunso mudzatonthozedwa.+ Chivumbulutso 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ine Yohane mʼbale wanu, amene mofanana ndi inu ndikupirira,+ ndikukumana ndi masautso+ ndipo tidzalamulira limodzi mu ufumu+ monga otsatira a Yesu,+ ndinali pachilumba cha Patimo chifukwa cholankhula za Mulungu ndi kuchitira umboni za Yesu.
17 Choncho ngati tili ana, ndifenso olandira cholowa kuchokera kwa Mulungu. Koma ndifenso olandira cholowa+ anzake a Khristu, ngati tikuvutika naye limodzi+ kuti tikalandire naye ulemerero.+
7 Chiyembekezo chathu pa inu sichikugwedezeka, chifukwa tikudziwa kuti popeza mukukumana ndi mavuto ofanana ndi amene ifeyo tikukumana nawo, nanunso mudzatonthozedwa.+
9 Ine Yohane mʼbale wanu, amene mofanana ndi inu ndikupirira,+ ndikukumana ndi masautso+ ndipo tidzalamulira limodzi mu ufumu+ monga otsatira a Yesu,+ ndinali pachilumba cha Patimo chifukwa cholankhula za Mulungu ndi kuchitira umboni za Yesu.