Maliko 11:9, 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno amene anali patsogolo komanso amene ankabwera mʼmbuyo ankafuula kuti: “Mʼpulumutseni!+ Wodalitsidwa ndi amene akubwera mʼdzina la Yehova!*+ 10 Wodalitsidwa ndi Ufumu wa atate wathu Davide+ umene ukubwerawo! Mʼpulumutseni kumwambamwambako!”
9 Ndiyeno amene anali patsogolo komanso amene ankabwera mʼmbuyo ankafuula kuti: “Mʼpulumutseni!+ Wodalitsidwa ndi amene akubwera mʼdzina la Yehova!*+ 10 Wodalitsidwa ndi Ufumu wa atate wathu Davide+ umene ukubwerawo! Mʼpulumutseni kumwambamwambako!”