Mateyu 21:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Komabe ngakhale kuti ankafuna kumugwira,* ankaopa gulu la anthu chifukwa anthuwo ankakhulupirira kuti iye ndi mneneri.+ Luka 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ataona zimenezi anthu onse anachita mantha ndipo anayamba kutamanda Mulungu kuti: “Mneneri wamkulu waonekera pakati pathu.”+ Ananenanso kuti, “Mulungu wakumbukira anthu ake.”+ Luka 24:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iye anawafunsa kuti: “Zinthu zake ziti?” Iwo anamuuza kuti: “Zinthu zokhudza Yesu Mnazareti,+ amene anali mneneri wamphamvu mʼzochita komanso mʼmawu pamaso pa Mulungu ndi anthu onse.+
46 Komabe ngakhale kuti ankafuna kumugwira,* ankaopa gulu la anthu chifukwa anthuwo ankakhulupirira kuti iye ndi mneneri.+
16 Ataona zimenezi anthu onse anachita mantha ndipo anayamba kutamanda Mulungu kuti: “Mneneri wamkulu waonekera pakati pathu.”+ Ananenanso kuti, “Mulungu wakumbukira anthu ake.”+
19 Iye anawafunsa kuti: “Zinthu zake ziti?” Iwo anamuuza kuti: “Zinthu zokhudza Yesu Mnazareti,+ amene anali mneneri wamphamvu mʼzochita komanso mʼmawu pamaso pa Mulungu ndi anthu onse.+