Mateyu 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Asiyeni amenewo. Iwo ndi atsogoleri akhungu. Choncho ngati munthu wakhungu akutsogolera wakhungu mnzake, onse awiri adzagwera mʼdzenje.”+
14 Asiyeni amenewo. Iwo ndi atsogoleri akhungu. Choncho ngati munthu wakhungu akutsogolera wakhungu mnzake, onse awiri adzagwera mʼdzenje.”+