12 Choncho iye ananena kuti: “Munthu wina wa mʼbanja lachifumu ankakonzekera kuti apite kudziko lakutali+ kuti akalandire ufumu nʼkubwerako. 13 Ndiyeno anaitana akapolo ake 10 nʼkuwapatsa ndalama zokwana ma mina 10 ndipo anawauza kuti, ‘Muchite malonda ndi ndalamazi mpaka nditabwera.’+