Aheberi 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musaiwale kuchereza alendo,*+ chifukwa pochita zimenezi, ena anachereza angelo mosadziwa.+ 3 Yohane 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wokondedwa, ukusonyeza kuti ndiwe wokhulupirika pa chilichonse chimene ukuchitira abale, ngakhale amene sukuwadziwa nʼkomwe.+
5 Wokondedwa, ukusonyeza kuti ndiwe wokhulupirika pa chilichonse chimene ukuchitira abale, ngakhale amene sukuwadziwa nʼkomwe.+