Miyambo 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Amene amakomera mtima munthu wonyozeka akukongoza Yehova,+Ndipo adzamʼbwezera* zimene anachitazo.+ Mateyu 10:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Amene wakulandirani walandiranso ine ndipo amene walandira ine walandiranso amene anandituma.+ Maliko 9:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Komanso aliyense amene wakupatsani kapu ya madzi akumwa chifukwa chakuti ndinu ophunzira a Khristu,+ ndithu ndikukuuzani, ameneyo mphoto yake sidzatayika.+ Aheberi 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa Mulungu si wosalungama kuti angaiwale ntchito yanu ndiponso chikondi chimene munachisonyeza pa dzina lake,+ potumikira oyera ndipo mukupitiriza kuwatumikira.
17 Amene amakomera mtima munthu wonyozeka akukongoza Yehova,+Ndipo adzamʼbwezera* zimene anachitazo.+
41 Komanso aliyense amene wakupatsani kapu ya madzi akumwa chifukwa chakuti ndinu ophunzira a Khristu,+ ndithu ndikukuuzani, ameneyo mphoto yake sidzatayika.+
10 Chifukwa Mulungu si wosalungama kuti angaiwale ntchito yanu ndiponso chikondi chimene munachisonyeza pa dzina lake,+ potumikira oyera ndipo mukupitiriza kuwatumikira.