Nehemiya 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Akalonga a anthuwo ankakhala ku Yerusalemu.+ Anthu ena onse anachita maere+ kuti apeze munthu mmodzi pa anthu 10 alionse woti akakhale ku Yerusalemu, mzinda woyera, ndipo anthu 9 otsalawo ankakhala mʼmizinda ina. Yesaya 52:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Dzuka! Dzuka! Vala mphamvu+ iwe Ziyoni.+ Vala zovala zako zokongola+ iwe Yerusalemu, mzinda woyera. Chifukwa munthu wosadulidwa ndi wodetsedwa sadzabweranso mwa iwe.+
11 Akalonga a anthuwo ankakhala ku Yerusalemu.+ Anthu ena onse anachita maere+ kuti apeze munthu mmodzi pa anthu 10 alionse woti akakhale ku Yerusalemu, mzinda woyera, ndipo anthu 9 otsalawo ankakhala mʼmizinda ina.
52 Dzuka! Dzuka! Vala mphamvu+ iwe Ziyoni.+ Vala zovala zako zokongola+ iwe Yerusalemu, mzinda woyera. Chifukwa munthu wosadulidwa ndi wodetsedwa sadzabweranso mwa iwe.+