Mateyu 26:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Anthu amene anagwira Yesu aja anapita naye kwa Kayafa+ mkulu wa ansembe, kumene alembi ndi akulu anali atasonkhana.+ Luka 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mʼmasiku amenewo Anasi anali wansembe wamkulu ndipo Kayafa+ anali mkulu wa ansembe. Pa nthawiyo mawu a Mulungu anafika kwa Yohane+ mwana wa Zekariya mʼchipululu.+ Yohane 11:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Koma mmodzi wa iwo, Kayafa,+ amene anali mkulu wa ansembe chaka chimenecho, anati: “Palibe chimene mukudziwa inu Yohane 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choyamba anapita naye kwa Anasi, chifukwa anali mpongozi wa Kayafa,+ amene anali mkulu wa ansembe chaka chimenecho.+ Yohane 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako Anasi anatumiza Yesu kwa Kayafa mkulu wa ansembe ndipo anali atamumanga.+
57 Anthu amene anagwira Yesu aja anapita naye kwa Kayafa+ mkulu wa ansembe, kumene alembi ndi akulu anali atasonkhana.+
2 Mʼmasiku amenewo Anasi anali wansembe wamkulu ndipo Kayafa+ anali mkulu wa ansembe. Pa nthawiyo mawu a Mulungu anafika kwa Yohane+ mwana wa Zekariya mʼchipululu.+
49 Koma mmodzi wa iwo, Kayafa,+ amene anali mkulu wa ansembe chaka chimenecho, anati: “Palibe chimene mukudziwa inu
13 Choyamba anapita naye kwa Anasi, chifukwa anali mpongozi wa Kayafa,+ amene anali mkulu wa ansembe chaka chimenecho.+