Luka 22:21-23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma taonani! Wondipereka ndili naye limodzi patebulo pompano.+ 22 Chifukwa Mwana wa munthu achoka mogwirizana ndi zimene zinanenedweratu.+ Koma tsoka kwa munthu amene akumupereka!”+ 23 Choncho anayamba kukambirana pakati pawo za amene anakonza chiwembu chimenecho.+ Yohane 6:70 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 70 Yesu anawauza kuti: “Ine ndinakusankhani inu 12, si choncho?+ Komatu mmodzi wa inu ndi wonenera anzake zoipa.”*+ Yohane 13:21, 22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Atanena zimenezi, Yesu anavutika kwambiri mumtima, ndipo anachitira umboni kuti: “Ndithu ndikukuuzani, mmodzi wa inu andipereka.”+ 22 Ophunzirawo anayamba kuyangʼanizana chifukwa sankadziwa kuti akunena ndani.+
21 Koma taonani! Wondipereka ndili naye limodzi patebulo pompano.+ 22 Chifukwa Mwana wa munthu achoka mogwirizana ndi zimene zinanenedweratu.+ Koma tsoka kwa munthu amene akumupereka!”+ 23 Choncho anayamba kukambirana pakati pawo za amene anakonza chiwembu chimenecho.+
70 Yesu anawauza kuti: “Ine ndinakusankhani inu 12, si choncho?+ Komatu mmodzi wa inu ndi wonenera anzake zoipa.”*+
21 Atanena zimenezi, Yesu anavutika kwambiri mumtima, ndipo anachitira umboni kuti: “Ndithu ndikukuuzani, mmodzi wa inu andipereka.”+ 22 Ophunzirawo anayamba kuyangʼanizana chifukwa sankadziwa kuti akunena ndani.+