Maliko 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwana wa munthu achoka, mogwirizana ndi zimene Malemba amanena za iye. Koma tsoka kwa munthu amene akupereka Mwana wa munthu!+ Zikanakhala bwino kwa munthu ameneyu ngati akanapanda kubadwa.”+
21 Mwana wa munthu achoka, mogwirizana ndi zimene Malemba amanena za iye. Koma tsoka kwa munthu amene akupereka Mwana wa munthu!+ Zikanakhala bwino kwa munthu ameneyu ngati akanapanda kubadwa.”+