Ekisodo 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Mose anatenga magaziwo nʼkuwaza anthuwo,+ ndipo anati: “Awa ndi magazi a pangano limene Yehova wapangana nanu mogwirizana ndi mawu onsewa.”+ Yeremiya 31:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Taonani! Masiku akubwera, pamene ndidzachita pangano latsopano ndi nyumba ya Isiraeli komanso nyumba ya Yuda,” akutero Yehova.+ Aheberi 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mogwirizana ndi zimenezi, Yesu wakhala chikole cha pangano labwino kwambiri.+
8 Choncho Mose anatenga magaziwo nʼkuwaza anthuwo,+ ndipo anati: “Awa ndi magazi a pangano limene Yehova wapangana nanu mogwirizana ndi mawu onsewa.”+
31 “Taonani! Masiku akubwera, pamene ndidzachita pangano latsopano ndi nyumba ya Isiraeli komanso nyumba ya Yuda,” akutero Yehova.+