Luka 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma gulu lonse linafuula kuti: “Ameneyu muthane naye basi, koma ife mutimasulire Baraba!”+ Yohane 18:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Anthuwo anafuulanso kuti: “Ameneyo ayi, koma Baraba!” Komatu Baraba ameneyu anali wachifwamba.+ Machitidwe 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inde, inu munakana woyera ndi wolungamayo, ndipo munapempha kuti akumasulireni munthu wopha anthu.+
14 Inde, inu munakana woyera ndi wolungamayo, ndipo munapempha kuti akumasulireni munthu wopha anthu.+