-
Maliko 15:22-24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Choncho anafika naye pamalo otchedwa Gologota. Liwuli akalimasulira limatanthauza, “Malo a Chibade.”+ 23 Kumeneko anayesa kumupatsa vinyo wosakaniza ndi mule,+ koma iye anakana. 24 Ndipo anamukhomerera pamtengo nʼkugawana malaya ake akunja pochita maere pa malayawo, kuti aone chimene munthu aliyense angatenge.+
-