Mateyu 26:60, 61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Koma sanaupeze ngakhale kuti kunabwera mboni zambiri zabodza.+ Patapita nthawi, kunabwera mboni zina ziwiri 61 nʼkunena kuti: “Munthu ameneyu ananena kuti, ‘Ndikhoza kugwetsa kachisi wa Mulungu nʼkumumanganso mʼmasiku atatu.’”+ Yohane 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yesu anawayankha kuti: “Gwetsani kachisiyu ndipo ine ndidzamumanga mʼmasiku atatu.”+
60 Koma sanaupeze ngakhale kuti kunabwera mboni zambiri zabodza.+ Patapita nthawi, kunabwera mboni zina ziwiri 61 nʼkunena kuti: “Munthu ameneyu ananena kuti, ‘Ndikhoza kugwetsa kachisi wa Mulungu nʼkumumanganso mʼmasiku atatu.’”+