Luka 23:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndiyeno mmodzi wa zigawenga zimene zinapachikidwa naye limodzi zija, anayamba kumulankhulira zachipongwe+ kuti: “Kodi si iwe Khristu? Dzipulumutse wekha, limodzi ndi ife.”
39 Ndiyeno mmodzi wa zigawenga zimene zinapachikidwa naye limodzi zija, anayamba kumulankhulira zachipongwe+ kuti: “Kodi si iwe Khristu? Dzipulumutse wekha, limodzi ndi ife.”