Luka 8:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Koma anthu onse ankalira komanso kudziguguda pachifuwa chifukwa cha chisoni. Choncho Yesu anawauza kuti: “Tontholani,+ chifukwa mwanayu sanamwalire, koma akugona.”+ Yohane 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atanena zimenezi, anauza ophunzira akewo kuti: “Mnzathu Lazaro ali mʼtulo,+ koma ndikupita kumeneko kukamudzutsa.”
52 Koma anthu onse ankalira komanso kudziguguda pachifuwa chifukwa cha chisoni. Choncho Yesu anawauza kuti: “Tontholani,+ chifukwa mwanayu sanamwalire, koma akugona.”+
11 Atanena zimenezi, anauza ophunzira akewo kuti: “Mnzathu Lazaro ali mʼtulo,+ koma ndikupita kumeneko kukamudzutsa.”