Luka 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako anthu okwana 70 aja anabwerera akusangalala ndipo anauza Yesu kuti: “Ambuye, ngakhale ziwanda zimatigonjera tikagwiritsa ntchito dzina lanu.”+
17 Kenako anthu okwana 70 aja anabwerera akusangalala ndipo anauza Yesu kuti: “Ambuye, ngakhale ziwanda zimatigonjera tikagwiritsa ntchito dzina lanu.”+