Mateyu 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yesu atatsika mʼngalawayo anaona gulu lalikulu la anthu ndipo anawamvera chisoni+ nʼkuwachiritsira anthu awo odwala.+ Aheberi 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chifukwa mkulu wa ansembe amene tili nayeyu, si mkulu wa ansembe amene sangatimvere chisoni pa zofooka zathu.+ Koma ndi mkulu wa ansembe amene anayesedwa pa zinthu zonse ngati ifeyo, ndipo anakhalabe wopanda uchimo.+
14 Yesu atatsika mʼngalawayo anaona gulu lalikulu la anthu ndipo anawamvera chisoni+ nʼkuwachiritsira anthu awo odwala.+
15 Chifukwa mkulu wa ansembe amene tili nayeyu, si mkulu wa ansembe amene sangatimvere chisoni pa zofooka zathu.+ Koma ndi mkulu wa ansembe amene anayesedwa pa zinthu zonse ngati ifeyo, ndipo anakhalabe wopanda uchimo.+