Mateyu 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma nthawi yomweyo Yesu anawauza kuti: “Mtima mʼmalo, ndine. Musachite mantha.”+ Yohane 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Yesu anawauza kuti: “Ndine, musachite mantha!”+