Maliko 6:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Ndipo akangolowa mʼmidzi kapena mʼmizinda komanso mʼmadera ozungulira, anthu ankakhazika odwala mʼmisika. Iwo ankamuchonderera kuti angogwira ulusi wopota wamʼmphepete mwa malaya ake akunja,+ ndipo anthu onse amene anaugwira anachira.
56 Ndipo akangolowa mʼmidzi kapena mʼmizinda komanso mʼmadera ozungulira, anthu ankakhazika odwala mʼmisika. Iwo ankamuchonderera kuti angogwira ulusi wopota wamʼmphepete mwa malaya ake akunja,+ ndipo anthu onse amene anaugwira anachira.