Yesaya 66:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Iwo adzapita kukaona mitembo ya anthu amene anandipandukira.Chifukwa mphutsi zodya mitemboyo sizidzafa.Komanso moto umene ukuiwotcha sudzazimitsidwa,+Ndipo idzakhala chinthu chonyansa kwa anthu onse.”
24 “Iwo adzapita kukaona mitembo ya anthu amene anandipandukira.Chifukwa mphutsi zodya mitemboyo sizidzafa.Komanso moto umene ukuiwotcha sudzazimitsidwa,+Ndipo idzakhala chinthu chonyansa kwa anthu onse.”