Mateyu 19:25, 26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ophunzirawo atamva zimenezi, anadabwa kwambiri ndipo anafunsa kuti: “Ndiye angapulumuke ndi ndani?”+ 26 Yesu anawayangʼanitsitsa nʼkuwauza kuti: “Kwa anthu zimenezi nʼzosatheka, koma zinthu zonse nʼzotheka kwa Mulungu.”+ Luka 18:26, 27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Amene anamva zimenezi anafunsa kuti: “Ndiye angapulumuke ndi ndani?”+ 27 Iye anawauza kuti: “Zinthu zosatheka kwa anthu nʼzotheka kwa Mulungu.”+
25 Ophunzirawo atamva zimenezi, anadabwa kwambiri ndipo anafunsa kuti: “Ndiye angapulumuke ndi ndani?”+ 26 Yesu anawayangʼanitsitsa nʼkuwauza kuti: “Kwa anthu zimenezi nʼzosatheka, koma zinthu zonse nʼzotheka kwa Mulungu.”+
26 Amene anamva zimenezi anafunsa kuti: “Ndiye angapulumuke ndi ndani?”+ 27 Iye anawauza kuti: “Zinthu zosatheka kwa anthu nʼzotheka kwa Mulungu.”+