Aroma 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Muzipereka kwa onse zimene amafuna. Amene amafuna msonkho, mʼpatseni msonkho.+ Amene amafuna ndalama ya chiphaso, mʼpatseni ndalama ya chiphaso. Amene amafuna kuopedwa, muopeni.+ Amene amafuna kupatsidwa ulemu, mʼpatseni ulemu wake.+ Tito 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pitiriza kuwakumbutsa kuti azigonjera ndiponso kumvera maboma ndi olamulira.+ Akhalenso okonzeka kugwira ntchito iliyonse yabwino. 1 Petulo 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Muzichita zimene Ambuye amafuna pogonjera ulamuliro uliwonse wokhazikitsidwa ndi anthu.+ Muzigonjera mfumu+ chifukwa ili ndi udindo waukulu,
7 Muzipereka kwa onse zimene amafuna. Amene amafuna msonkho, mʼpatseni msonkho.+ Amene amafuna ndalama ya chiphaso, mʼpatseni ndalama ya chiphaso. Amene amafuna kuopedwa, muopeni.+ Amene amafuna kupatsidwa ulemu, mʼpatseni ulemu wake.+
3 Pitiriza kuwakumbutsa kuti azigonjera ndiponso kumvera maboma ndi olamulira.+ Akhalenso okonzeka kugwira ntchito iliyonse yabwino.
13 Muzichita zimene Ambuye amafuna pogonjera ulamuliro uliwonse wokhazikitsidwa ndi anthu.+ Muzigonjera mfumu+ chifukwa ili ndi udindo waukulu,