2 Samueli 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mzimu wa Yehova unalankhula kudzera mwa ine;+Mawu ake anali palilime langa.+ 2 Timoteyo 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Malemba onse anauziridwa ndi Mulungu,+ ndipo ndi othandiza pophunzitsa,+ kudzudzula, kukonza zinthu ndi kulangiza mwachilungamo,+ 2 Petulo 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa ulosi sunachokere kwa anthu,+ koma anthuwo analankhula mawu ochokera kwa Mulungu motsogoleredwa* ndi mzimu woyera.+
16 Malemba onse anauziridwa ndi Mulungu,+ ndipo ndi othandiza pophunzitsa,+ kudzudzula, kukonza zinthu ndi kulangiza mwachilungamo,+
21 Chifukwa ulosi sunachokere kwa anthu,+ koma anthuwo analankhula mawu ochokera kwa Mulungu motsogoleredwa* ndi mzimu woyera.+