8 Nditayangʼana, ndinaona hatchi yotuwa. Amene anakwera pahatchiyi dzina lake anali Imfa. Ndipo Manda ankamutsatira pafupi kwambiri. Iwo anapatsidwa ulamuliro pa gawo limodzi la magawo 4 adziko lapansi, kuti aphe anthu ndi lupanga lalitali, njala,+ mliri woopsa komanso zilombo zapadziko lapansi.+