-
Yesaya 51:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Kwezani maso anu kumwamba,
Ndipo yangʼanani padziko lapansi.
Kumwamba kudzabenthukabenthuka nʼkumwazika ngati utsi,
Dziko lapansi lidzatha ngati chovala,
Ndipo anthu amene akukhala mmenemo adzafa ngati ntchentche.
-