Luka 21:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho khalani maso+ ndipo muzipemphera mopembedzera nthawi zonse,+ kuti mudzathe kuthawa zinthu zonsezi zimene zikuyenera kuchitika, komanso kuti mudzathe kuima pamaso pa Mwana wa munthu.”+
36 Choncho khalani maso+ ndipo muzipemphera mopembedzera nthawi zonse,+ kuti mudzathe kuthawa zinthu zonsezi zimene zikuyenera kuchitika, komanso kuti mudzathe kuima pamaso pa Mwana wa munthu.”+