-
Mateyu 27:46-49Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
46 Cha mʼma 3 kolokomo, Yesu anafuula mwamphamvu kuti: “Eʹli, Eʹli, laʹma sa·bach·thaʹni?” kutanthauza kuti, “Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?”+ 47 Ena mwa anthu amene anaimirira chapomwepo atamva zimenezi anayamba kunena kuti: “Munthuyu akuitana Eliya.”+ 48 Nthawi yomweyo mmodzi wa iwo anathamanga kukatenga siponji nʼkuiviika muvinyo wowawasa ndipo anaiika kubango nʼkumupatsa kuti amwe.+ 49 Koma enawo anati: “Mulekeni! Tione ngati Eliya angabwere kudzamupulumutsa.”
-