Maliko 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pomaliza, mbewu zimene zinafesedwa panthaka yabwino ndi anthu amene amamvetsera mawu ndipo amawalandira bwino nʼkubereka zipatso wina 30, wina 60 ndipo wina 100.”+
20 Pomaliza, mbewu zimene zinafesedwa panthaka yabwino ndi anthu amene amamvetsera mawu ndipo amawalandira bwino nʼkubereka zipatso wina 30, wina 60 ndipo wina 100.”+