-
Numeri 6:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 “Lankhula ndi Aisiraeli ndipo uwauze kuti, ‘Ngati mwamuna kapena mkazi wachita lonjezo lapadera kwa Yehova lokhala Mnaziri,*+ 3 asamamwe vinyo ndi zakumwa zina zoledzeretsa. Asamamwenso viniga* wokhala ndi vinyo, kapena viniga wochokera ku zakumwa zina zoledzeretsa,+ kapenanso madzi a mphesa. Ndiponso asamadye mphesa zaziwisi kapena zouma.
-
-
Mateyu 11:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Mofanana ndi zimenezi, Yohane anabwera ndipo sankadya kapena kumwa. Koma anthu ankanena kuti, ‘Ali ndi chiwanda.’
-