Genesis 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mwanayo anamupatsa dzina lakuti Nowa,*+ ndipo anati: “Uyu ndi amene adzatibweretsere mpumulo ku ntchito yathu yovuta komanso yopweteketsa manja, chifukwa cholima nthaka imene Yehova anaitemberera.”+
29 Mwanayo anamupatsa dzina lakuti Nowa,*+ ndipo anati: “Uyu ndi amene adzatibweretsere mpumulo ku ntchito yathu yovuta komanso yopweteketsa manja, chifukwa cholima nthaka imene Yehova anaitemberera.”+