2 Koma patapita masiku angapo, Yesu analowanso mu Kaperenao ndipo anthu anamva kuti ali panyumba.+ 2 Choncho anthu ambiri anasonkhana kumeneko moti panalibenso malo okhala, chifukwa anthu anadzaza mpaka pakhomo ndipo anayamba kuwauza uthenga wabwino.+