Mateyu 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma iwe ukamapemphera, uzilowa mʼchipinda chako nʼkutseka chitseko ndipo uzipemphera kwa Atate wako amene sungathe kuwaona.+ Ukatero Atate wako amene akuona zimene zikuchitika ngakhale kuti iweyo sungathe kuwaona, adzakubwezera. Maliko 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako anakwera phiri nʼkuitana anthu amene ankawafuna+ ndipo iwo anapita kwa iye.+
6 Koma iwe ukamapemphera, uzilowa mʼchipinda chako nʼkutseka chitseko ndipo uzipemphera kwa Atate wako amene sungathe kuwaona.+ Ukatero Atate wako amene akuona zimene zikuchitika ngakhale kuti iweyo sungathe kuwaona, adzakubwezera.