Machitidwe 7:59, 60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Pamene ankamuponya miyala, Sitefano anapempha mochonderera kuti: “Ambuye Yesu, landirani mzimu wanga.” 60 Kenako anagwada nʼkufuula ndi mawu amphamvu kuti: “Yehova,* musawaimbe mlandu wa tchimo ili.”+ Atanena zimenezi anafa.* Aroma 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pitirizani kudalitsa anthu amene akukuzunzani.+ Muzidalitsa, osati kutemberera.+
59 Pamene ankamuponya miyala, Sitefano anapempha mochonderera kuti: “Ambuye Yesu, landirani mzimu wanga.” 60 Kenako anagwada nʼkufuula ndi mawu amphamvu kuti: “Yehova,* musawaimbe mlandu wa tchimo ili.”+ Atanena zimenezi anafa.*