Maliko 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yesu atawolokanso pangalawa kubwerera kutsidya lina, gulu lalikulu la anthu linasonkhana kwa iye, pa nthawiyi iye anali mʼmphepete mwa nyanja.+
21 Yesu atawolokanso pangalawa kubwerera kutsidya lina, gulu lalikulu la anthu linasonkhana kwa iye, pa nthawiyi iye anali mʼmphepete mwa nyanja.+