5 Mulungu woona Yehova,
Amene analenga kumwamba ndiponso Mulungu Wamkulu amene anakutambasula,+
Amene anapanga dziko lapansi ndi zonse zimene zili mmenemo,+
Amene amapereka mpweya kwa anthu amene ali mmenemo,+
Komanso mzimu kwa anthu amene amayenda padzikolo,+ wanena kuti: