2 Mbiri 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Maso a Yehova akuyendayenda padziko lonse lapansi+ kuti aonetse mphamvu zake* kwa anthu odzipereka ndi mtima wonse kwa iye.*+ Mwachita zopusa pa nkhani imeneyi. Kuyambira pano mʼdziko lanu muzichitika nkhondo.”+ Afilipi 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chifukwa cha zimenezi, Mulungu wanga adzakupatsani zonse zimene mukufunikira+ mogwirizana ndi kuchuluka kwa chuma chake chaulemerero, kudzera mwa Khristu Yesu.
9 Maso a Yehova akuyendayenda padziko lonse lapansi+ kuti aonetse mphamvu zake* kwa anthu odzipereka ndi mtima wonse kwa iye.*+ Mwachita zopusa pa nkhani imeneyi. Kuyambira pano mʼdziko lanu muzichitika nkhondo.”+
19 Chifukwa cha zimenezi, Mulungu wanga adzakupatsani zonse zimene mukufunikira+ mogwirizana ndi kuchuluka kwa chuma chake chaulemerero, kudzera mwa Khristu Yesu.