Yohane 5:28, 29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musadabwe nazo zimenezi, chifukwa nthawi ikubwera imene onse amene ali mʼmanda achikumbutso adzamva mawu ake+ 29 ndipo adzatuluka. Amene ankachita zabwino adzauka kuti alandire moyo ndipo amene ankachita zoipa adzauka kuti aweruzidwe.+ Yohane 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Marita anati: “Ndikudziwa kuti adzauka pa kuuka kwa akufa+ mʼtsiku lomaliza.” Machitidwe 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo ine ndili ndi chiyembekezo ngati chimenenso anthu awa ali nacho, kuti Mulungu adzaukitsa+ olungama ndi osalungama omwe.+
28 Musadabwe nazo zimenezi, chifukwa nthawi ikubwera imene onse amene ali mʼmanda achikumbutso adzamva mawu ake+ 29 ndipo adzatuluka. Amene ankachita zabwino adzauka kuti alandire moyo ndipo amene ankachita zoipa adzauka kuti aweruzidwe.+
15 Ndipo ine ndili ndi chiyembekezo ngati chimenenso anthu awa ali nacho, kuti Mulungu adzaukitsa+ olungama ndi osalungama omwe.+